2 Mbiri 3:15 BL92

15 Ndipo anapanga ku khomo la nyumba nsanamira ziwiri za mikono makumi atatu mphambu ziwiri; ndi mutu unakhala pamwamba pa iri yonse ndiwo mikono isanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 3

Onani 2 Mbiri 3:15 nkhani