2 Mbiri 30:26 BL92

26 Momwemo munali cimwemwe cacikuru m'Yerusalemu; pakuti kuyambira masiku a Solomo mwana wa Davide mfumu ya Israyeli simunacitika cotero m'Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:26 nkhani