2 Mbiri 30:8 BL92

8 Musamakhala ouma khosi monga makolo anu; koma gwiranani dzanja ndi Yehova, nimulowe m'malo ace opatulika, amene anapatula kosatha, ndi kutumikira Yehova Mulungu wanu; kuti mkwiyo wace waukali utembenuke kwa inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 30

Onani 2 Mbiri 30:8 nkhani