2 Mbiri 31:2 BL92

2 Ndipo Hezekiya anaika zigawo za ansembe ndi Alevi, monga mwa magawidwe ao, yense monga mwa utumiki wace, ndi ansembe ndi Alevi, acite nsembe zopsereza ndi nsembe zoyamika kutumikira, ndi kuyamika, ndi kulemekeza, ku zipata za cigono ca Ambuye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 31

Onani 2 Mbiri 31:2 nkhani