2 Mbiri 31:8 BL92

8 Ndipo pamene Hezekiya ndi akuru ace anadza, naona miyuruyi, analemekeza Yehova, nadalitsa anthu ace Aisrayeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 31

Onani 2 Mbiri 31:8 nkhani