18 Ndipo anapfuula ndi mau akuru m'cinenedwe ca Ayuda kwa anthu a m'Yerusalemu okhala palinga, kuwaopsa ndi kuwabvuta, kuti alande mudziwu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32
Onani 2 Mbiri 32:18 nkhani