2 Mbiri 32:20 BL92

20 Ndipo Hezekiya mfumu, ndi Yesaya mneneri mwana wa Amozi, anapemphera pa ici, napfuulira Kumwamba.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32

Onani 2 Mbiri 32:20 nkhani