24 Masiku omwe aja Hezekiya anadwala pafupi imfa; ndipo anapemphera kwa Yehova; ndi Iye ananena naye, nampatsa cizindikilo codabwiza.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32
Onani 2 Mbiri 32:24 nkhani