5 Ndipo analimbika mtima, namangitsa linga lonse mopasuka, nalikweza mpaka pansanja, ndi linga lina kunja kwace, nalimbitsa Milo m'mudzi wa Davide, napanga zida ndi zikopa zocuruka.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 32
Onani 2 Mbiri 32:5 nkhani