22 Ndipo anacita coipa pamaso pa Yehova, monga umo anacitira Manase atate wace; pakuti Amoni anaphera nsembe mafano osema onse amene adawapanga Manase atate wace, nawatumikira.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:22 nkhani