3 Pakuti anamanganso misanje adaipasula Hezekiya atate wace, nautsira Abaala maguwa a nsembe, napanga zifanizo, nalambira khamu lonse la kuthambo, nalitumikira.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:3 nkhani