9 Koma Manase analakwitsa Yuda ndi okhala m'Yerusalemu, kotero kuti anacita coipa koposa amitundu, amene Yehova anawaononga pamaso pa ana a Israyeli.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 33
Onani 2 Mbiri 33:9 nkhani