2 Mbiri 34:21 BL92

21 Mukani, mundifunsire kwa Yehova, ine ndi otsala m'Israyeli ndi Yuda, za mau a m'buku lopezekalo; pakuti ukali wa Yehova atitsanulirawu ndi waukuru; popeza makolo athu sanasunga mau a Yehova kucita monga mwa zonse zolembedwa m'bukumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:21 nkhani