2 Mbiri 35:1 BL92

1 Pamenepo Yosiya anacitira Yehova Paskha m'Yerusalemu, naphera Paskha tsiku lakhumi ndi cinai la mwezi woyamba.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:1 nkhani