2 Mbiri 35:10 BL92

10 Momwemo anakonzera kutumikiraku, naima ansembe pokhala pao, ndi Alevi m'zigawo zao, monga umo adawauzira mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:10 nkhani