2 Mbiri 35:12 BL92

12 Ndipo anacotsapo nsembe zopsereza, kuti azipereke kwa ana a anthu monga mwa magawidwe a nyumba za makolo; azipereke kwa Yehova monga mulembedwa m'buku la Mose. Natero momwemo ndi ng'ombezo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:12 nkhani