20 Citatha ici conse, Yosiya atakonza nyumbayi, Neko mfumu ya Aigupto anakwera kuyambana ku Karikemisi ku Firate; ndipo Yosiya anamturukira kuyambana naye.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35
Onani 2 Mbiri 35:20 nkhani