2 Mbiri 35:25 BL92

25 Ndipo Yeremiya anamlembera Yosiya nyimbo yomlira; ndi oyimbira onse, amuna ndi akazi, amanena za Yosiya nyimbo za maliro zao mpaka lero lino; naziika zikhale lemba m'Israyeli; taonani, zilembedwa m'Nyimbo za Maliro.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 35

Onani 2 Mbiri 35:25 nkhani