16 koma ananyodola mithenga ya Mulungu, napeputsa mau ace, naseka aneneri ace, mpaka ukali wa Mulungu unaukira anthu ace, mpaka panalibe colanditsa.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36
Onani 2 Mbiri 36:16 nkhani