2 Mbiri 4:18 BL92

18 Ndipo Solomo anazipanga zipangizo izi zonse zocurukadi, pakuti kulemera kwace kwa mkuwa sikunayeseka.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 4

Onani 2 Mbiri 4:18 nkhani