2 Mbiri 4:5 BL92

5 Ndi kucindikira kwace kunanga cikhato, ndi mlomo wace unasadamuka ngati mlomo wa comwera, ngati luwa la kakombo; analowamo madzi a mitsuko yaikuru zikwi zitatu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 4

Onani 2 Mbiri 4:5 nkhani