8 Anapanganso magome khumi, nawaika m'Kacisi, asanu ku dzanja lamanja, ndi asanu ku dzanja lamanzere. Napanga mbale zowazira zana limodzi zagolidi.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 4
Onani 2 Mbiri 4:8 nkhani