10 Munalibe kanthu kena m'likasa, koma magome awiri Mose anawaika m'mwemo ku Horebu, muja Yehova anacita cipangano ndi ana a Israyeli poturuka iwo m'Aigupto.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 5
Onani 2 Mbiri 5:10 nkhani