2 Mbiri 5:2 BL92

2 Pamenepo Solomo anasonkhanitsira akulu akulu a Israyeli, ndi akuru onse a mafuko, ndi akalonga a nyumba za makolo a ana a Israyeli, ku Yerusalemu, kukatenga likasa la cipangano ca Yehova ku mudzi wa Davide ndiwo Zioni.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 5

Onani 2 Mbiri 5:2 nkhani