2 Mbiri 6:10 BL92

10 Ndipo Yehova wakhazikitsa mau ace adanenawo, pakuti ndinauka ine m'malo mwa Davide atate wanga, ndipo ndikhala pa mpando wacifumu wa Israyeli monga analonjeza Yehova, ndipo ndamangira dzina la Yehova Mulungu wa Israyeli nyumbayi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:10 nkhani