2 Mbiri 6:24 BL92

24 Ndipo anthu anu Israyeli akawakantha mdani cifukwa ca kukucimwirani, nakabwerera iwowa ndi kubvomereza dzina lanu, ndi kupemphera, ndi kupembedzera pamaso panu m'nyumba yino;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:24 nkhani