26 Mukatsekeka m'mwamba, mopanda mvula, cifukwa ca kukucimwirani; akapemphera iwo kuloza kumalo kuno, ndi kubvomereza dzina lanu, ndi kutembenuka kwa zoipa zao, pamene muwasautsa;
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6
Onani 2 Mbiri 6:26 nkhani