2 Mbiri 6:28 BL92

28 Mukakhala njala m'dzikomo, mukakhala mliri, mukakhala cinsikwi, kapena cinoni, dzombe, kapena kapuce; akawamangira misasa adani ao, m'dziko la midzi yao; mukakhala mliri uli wonse, kapena nthenda iri yonse;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:28 nkhani