41 Ndipo tsopano nyamukani, Yehova Mulungu, kudza kopumulira kwanu, Inu ndi likasa la mphamvu yanu; ansembe anu, Yehova Mulungu, abvale cipulumutso; ndi okondedwa anu akondwere nazo zabwino.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6
Onani 2 Mbiri 6:41 nkhani