2 Mbiri 6:8 BL92

8 Koma Yehova anati kwa Davide atate wanga, Popeza unafuna mumtima mwako kulimangira dzina langa nyumba, unacita bwino kuti unatero mumtima mwako;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:8 nkhani