2 Mbiri 7:6 BL92

6 Naimirira ansembe m'udikiro wao; ndi Alevi omwe ndi zoyimbira za Yehova, adazipanga Davide mfumu kuyamika nazo Yehova, pakuti cifundo cace cikhala cikhalire, polemekeza Davide mwa utumiki wao; ndi ansembe anaomba malipenga pamaso pao, nakhala ciriri Israyeli yense.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 7

Onani 2 Mbiri 7:6 nkhani