8 Nthawi yomweyo Solomo anacita madyerero masiku asanu ndi awiri, ndi Aisrayeli onse pamodzi naye, khamu lalikuru ndithu, kuyambira polowera ku Hamati kufikira mtsinje wa ku Aigupto.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 7
Onani 2 Mbiri 7:8 nkhani