2 Mbiri 8:17 BL92

17 Pamenepo Solomo anamuka ku Ezioni Geberi, ndi ku Eloti pambali pa nyanja, m'dziko la Edomu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 8

Onani 2 Mbiri 8:17 nkhani