2 Mbiri 8:6 BL92

6 ndi Balati, ndi midzi yonse yosungiramo cuma anali nayo Solomo, ndi midzi yonse ya magareta ace, ndi midzi ya apakavalo ace, ndi zonse anazifuna Solomo kuzimanga zomkondweretsa m'Yerusalemu, ndi m'Lebano, ndi m'dziko lonse la ufumu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 8

Onani 2 Mbiri 8:6 nkhani