2 Mbiri 9:27 BL92

27 Ndipo mfumu inacurukitsa siliva m'Yerusalemu ngati miyala; ndi mikungudza anailinganiza ndi mikuyu iri kumadambo kucuruka kwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 9

Onani 2 Mbiri 9:27 nkhani