9 Tsopano, Yehova Mulungu, likhazikike lonjezano lanu la kwa Davide atate wanga; pakuti mwandiika mfumu ya anthu akucuruka ngati pfumbi lapansi.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 1
Onani 2 Mbiri 1:9 nkhani