2 Mbiri 11:4 BL92

4 Atero Yehova, Musamuka kukayambana ndi abale anu, bwererani yense ku nyumba yace; pakuti cinthu ici cifuma kwa Ine. Ndipo anamvera mau a Yehova, nabwerera osakayambana ndi Yerobiamu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 11

Onani 2 Mbiri 11:4 nkhani