2 Mbiri 13:3 BL92

3 Ndipo Abiya anayambana nkhondo ali ndi khamu la ngwazi za nkhondo, amuna osankhika zikwi mazana anai; Yerobiamu atandandalitsa nkhondo yace ilimbane naye ndi amuna osankhika zikwi mazana asanu ndi atatu, ndiwo ngwazi zamphamvu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 13

Onani 2 Mbiri 13:3 nkhani