2 Mbiri 13:2 BL92

2 Anakhala mfumu m'Yerusalemu zaka zitatu; ndi dzina la mace ndiye Mikaya mwana wamkazi wa Uriyeli wa ku Gibeya. Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobiamu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 13

Onani 2 Mbiri 13:2 nkhani