7 Ndipo anamsonkhanira amuna acabe, anthu opanda pace, ndiwo anadzilimbikitsa kutsutsana naye Rehabiamu mwana wa Solomo, muja Rehabiamu anali mnyamata ndi woolowa mtima, wosakhoza kuwalaka.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 13
Onani 2 Mbiri 13:7 nkhani