5 Cifukwa cace Yehova anakhazikitsa ufumuwo m'dzanja lace, ndi onse Ayuda anabwera nayo mitulo kwa Yehosafati; ndipo zidamcurukira cuma ndi ulemu.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 17
Onani 2 Mbiri 17:5 nkhani