2 Mbiri 18:7 BL92

7 Ndipo mfumu ya Israyeli inati kwa Yehosafati, Atsalanso munthu mmodzi, tifunsire Yehova kwa iye; koma ndimuda, pakuti sandinenera ine kanthu kokoma, koma zoipa nthawi zonse, ndiye Mikaya mwana wa Yimla. Nati Yehosafati, Isatero mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 18

Onani 2 Mbiri 18:7 nkhani