2 Mbiri 20:21 BL92

21 Ndipo atafunsana ndi anthu, anaika oyimbira Yehova, ndi kulemekeza ciyero cokometsetsa, pakuturuka iwo kutsogolera khamu la nkhondo, ndi kuti, Yamikani Yehova, pakuti cifundo cace cikhala cosatha.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 20

Onani 2 Mbiri 20:21 nkhani