2 Mbiri 20:29 BL92

29 Ndipo kuopsa kwa Mulungu kunagwera maufumu onse a m'maiko, pamene anamva kuti Yehova adayambana ndi adani a Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 20

Onani 2 Mbiri 20:29 nkhani