2 Mbiri 20:5 BL92

5 Ndipo Yehosafati anaima mu msonkhano wa Ayuda, ndi a ku Yerusalemu, ku nyumba ya Yehova, pakati pa bwalo latsopano;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 20

Onani 2 Mbiri 20:5 nkhani