2 Mbiri 20:9 BL92

9 Cikatigwera coipa, lupanga, ciweruzo, kapena mliri, kapena njala, tidzakhala ciriri pakhomo pa nyumba iyi, ndi pamaso panu, (pakuti m'nyumba muno muli dzina lanu), ndi kupfuulira kwa Inu m'kusauka kwathu; ndipo mudzamvera ndi kulanditsa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 20

Onani 2 Mbiri 20:9 nkhani