2 Mbiri 22:2 BL92

2 Ahaziya anali wa zaka makumi anai mphambu ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu caka cimodzi; ndi dzina la mace ndiye Ataliya mwana wa Omri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 22

Onani 2 Mbiri 22:2 nkhani