2 Mbiri 23:9 BL92

9 Ndi Yehoyada wansembe anapereka kwa akazembe a mazana mikondo, ndi zikopa, ndi maraya acitsulo, zinali za mfumu Davide, zokhala m'nyumba, ya Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 23

Onani 2 Mbiri 23:9 nkhani