2 Mbiri 24:22 BL92

22 Motero mfumu Yoasi sanakumbukila zokoma anamcitirazi Yehoyada atate wace, koma anapha mwana wace; ndiye pomwalira anati, Yehova acipenye, nacifunse.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24

Onani 2 Mbiri 24:22 nkhani