27 Za ana ace tsono, ndi katundu wamkuru anamsenza, ndi kumanganso kwa nyumba ya Mulungu, taonani, zilembedwa m'buku lomasulira la mafumu. Ndipo Amaziya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.
Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 24
Onani 2 Mbiri 24:27 nkhani